Samurai jack🇲🇼 retweeted
Asin’ganga kukuuza kuti chizimba ndichozungulila nyumba kawili basitu wapenga misala.
Samurai jack🇲🇼 retweeted
Dating a baddie makes you a winner in men’s eyes but marrying her makes you a fool in their eyes. Make it make sense. 😂
Samurai jack🇲🇼 retweeted
I will never forget:
D - Diesel
P - Petrol
P - Palibe
Whoever coined this 🔥 This was too iconic.
Samurai jack🇲🇼 retweeted
Health center Ina ku kasungu anakhala 2 weeks opanda magetsi ati poti boma limakanika kugula ma units a magetsi (?)..Mpaka mwana wina anamwalira week yatha chifukwa cha vutoli. Lero a MP akumeneko aganiza zogula ma units a k100,000 kuti magetsi ayake. Zoopsa
Samurai jack🇲🇼 retweeted
This is the start of a dream for Keturah and I, a dream of September.
This is our story: youtu.be/onqzwoS4cgA?si=2-x1…
Samurai jack🇲🇼 retweeted
Mzimayi kumwalira ndithu. Nkhani yake? pa chipatala mafuta agalimoto palibe. Dziko lafikapo ili
koma chavala black mmh
Akazi A Kunja Samazimva Ngati Achimidzi Adzadza Kunowa Hmmm .Ndizomvesa Chisoni Kuwona Mkazi Wa Ku Malawi 🇲🇼 Akuzimva Koma Alibe Chilichonse 😖.#highlights #viralpost
158









































