DZiiiiiii retweeted
Ati ngati Ca$ino kulibe ndekuti Trap pangali.
Amene Trap ikumuvuta bola angoyamba chimntali.
Sindingamalimbane ndi munthu pano ndiku chaser imali.
Ndidzuke, ndi praisey, ndidye shower kenako wautali.
Ndingodya ka wawi, ka thobwa kozizira pa mbali.
-Ca$ino, 2026-
DZiiiiiii retweeted
Maybe it’s time to try Zomba huns, or even Mzuzu. Blantyre and Lilongwe huns have nothing to offer me😂😂
DZiiiiiii retweeted
Replying to @TibrahMw
Salary kungochotsapo ya Malawi gin muwiri, watsala kale ndiya tomato. 🤣




























