steve retweeted
Ambiri pano akudandaula za economy chifukwa anasiya kukhala ndimakolo awo😂😂akati awone ya rent, electricity bills,water bills, ya zakudya pompo kenako Ina yoti usangalale pa town pano ndalama sikukwana iyi 😂😂
steve retweeted
Nzika ya Malawi kuyifusa kuti “mutipo bwanji za situation ya dziko lanu m’mene ilili” akuti bola MCP inatuluka m’boma. Like really? That’s all you gotta say?😂
steve retweeted
No fuel. No forex. Corruption is choking the economy while the black market thrives. We deserve a President who speaks to the nation before we completely panic.
The current atmosphere is giving chilling echoes of the deadliest demonstrations we’ve seen in the past.
steve retweeted
Nnalidi ndi maganizo okwatira amuna awiri, koma ndi mmene dziko likuyenderamu,...hmmm Mmodzi yemweyu basi😩😩, Boma landionongera ma pulogalamu 😭💔
steve retweeted
Ku Malawi kunalowa chibwana when it comes to pricing of things. Aliyense akufuna kulemela pakamodzi 🤣🤣🤣
steve retweeted
Ndateleka nsima..ndaikandila..yabwata.. Ndisanayambe kutchakula, magetsi athima... ndati demeti...ndathira shuga ndingomwa phala...kenaka magetsi ayakaso...ah ah Escom, ineyo wamisala? Ndaitelekaso, ndaitchakula mwa nyoo...ndidya nsima yothira shuga lero. Mxiiew.
steve retweeted
Osamangoti Malawi needs Revolution. Tawafotokozereni bwinobwino a Malawi kuti revolution ndi chani mu chichewa chomveka so that we can all be on the same page.
steve retweeted
Just give @Dreamweave265 chance to be a main supplier! We can sort this within 30 days
steve retweeted
Thank you so much to AS Motors based in Blantyre, Nyambadwe!
Their contact: +265 988 71 18 71
steve retweeted
Kumukwatira mkazi chifukwa choti wampasa mimba zili ngati "Akulu mwaonongacho mugula"😂💔





















