Rejected handsome 🇲🇼🇿🇲🇿🇦 (@omex98) profile picture
Joined March 2024
Photo by Rejected handsome 🇲🇼🇿🇲🇿🇦 (@omex98)Photo by Rejected handsome 🇲🇼🇿🇲🇿🇦 (@omex98)Photo by Rejected handsome 🇲🇼🇿🇲🇿🇦 (@omex98)Photo by Rejected handsome 🇲🇼🇿🇲🇿🇦 (@omex98)Photo by Rejected handsome 🇲🇼🇿🇲🇿🇦 (@omex98)Photo by Rejected handsome 🇲🇼🇿🇲🇿🇦 (@omex98)Photo by Rejected handsome 🇲🇼🇿🇲🇿🇦 (@omex98)Photo by Rejected handsome 🇲🇼🇿🇲🇿🇦 (@omex98)Photo by Rejected handsome 🇲🇼🇿🇲🇿🇦 (@omex98)Photo by Rejected handsome 🇲🇼🇿🇲🇿🇦 (@omex98)
apa sizinayende, RIP Super Star
5
167
Komatu ichi chimaugeya mwano😂 chimvekere" pa 16 September paja pa ballot paja panali anyamata ambirimbiri koma a Malawi anasankh munthalika okalamba nde musamupaatse pressure munthalika kuti ayankhul(state of emergency) musiyeni azipuma"
68
Film ya SONA ndaonerako ma highlights ku page ya phwedo that film is realistic and is very sensitive to government ndipo ikukambadi ndende situation ilili pa Malawi pano, muli za Fuel, Amaryllis hotel, etc. NDLE aside kodi inuyo mukanalhala boma mukanayilola?
81
I think amuna awo awagwila ndi side chick😄
What's wrong with her?
60
I THINK WANKULUDI NDIMULUNGU, THE WAY HE IS FUCKIN THAT GRANNY IS SOMETHING ELSE
487
Misonkho ija osazaiphweketsa munthu akamadya amanenepa nayo, tawaoneni makosanawa ali ku opposition anali owonda ingakhale anali ndi ndalama kale koma kungolowaa mu bomamu achita kudumtukiratu, iii koma msonkho iwe😮‍💨
7
10
2
62
2,889
Kodi posinthira ma settings ku twitter kuno kuti ma videos asamazipange play okha ndipati? Ndinali mu Sana madzulo ano ndili pa mzere Olipila paja mix mnapqlanga follow page ya wild lagos zinangofikilatu pa chorus nde kumbuyo kwangaku kunali dona inayake kaya inaona kaya🫩
4
1,624
Paja ndikati ndiyankhuleko mutation ndine wa congress, koma moti izizi nzabwino?
People are in pain out here, and DPP leadership is failing miserably this crisis is deeper than we think
1
131
Mukandionera patali ndimaoneka ngati ndine opanda ndalama koma mukandiyandikila ndipomwe mungadziwe kuti ndalamazo ndilibedi🫩
4
235
Ingompangani follow nkazionera konko
Before I follow, somebody or herself let me know, is this chigoba or really her?
65
Zisakhale kuti amashowanatu chifukwa mu7 sanachenjere mongokumbutsana Samia paja ndi widow
68
Apapa timboleze anyamata a dpp wa zawavuta tisaname
45
Mtima olimbikila tilinawo koma vuto nkobadwira tsopano😮‍💨
1
2
125
Kumuchinda ma round 10 pati
unavailable
42
Am with her sikuti poti ndi kholo ndekuti ndi anzeru kuposa iweyo and it's not a must kuti tiziwamvera zilizonse
Kuchikakamiratu chiwalo 😂
48
Munthune ndine owonoka bwino ndithu. Zimangosowekera ndi ndalama kuti zinditsuke ndiwale🏃
54